Salimo 95:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamene makolo anu anandiyesa.+Iwo anatsutsana ndi ine ngakhale kuti anaona ntchito zanga.+