Salimo 96:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pamene amakhala pali ulemu ndi ulemerero.+Mphamvu ndi kukongola zili mʼnyumba yake yopatulika.+