Salimo 96:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mʼpatseni Yehova zimene akuyenera kulandira, inu mabanja a mitundu ya anthu,Mʼpatseni Yehova zimene akuyenera kulandira chifukwa cha ulemerero ndi mphamvu zake.+
7 Mʼpatseni Yehova zimene akuyenera kulandira, inu mabanja a mitundu ya anthu,Mʼpatseni Yehova zimene akuyenera kulandira chifukwa cha ulemerero ndi mphamvu zake.+