Salimo 96:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kumwamba kukondwere ndipo dziko lapansi lisangalale.Nyanja ichite mkokomo ndi zonse zimene zili mmenemo.+
11 Kumwamba kukondwere ndipo dziko lapansi lisangalale.Nyanja ichite mkokomo ndi zonse zimene zili mmenemo.+