Salimo 96:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mtunda ndi zonse zimene zili pamenepo zikondwere.+ Pa nthawi imodzimodziyo, mitengo yonse yamʼnkhalango ifuule mosangalala+
12 Mtunda ndi zonse zimene zili pamenepo zikondwere.+ Pa nthawi imodzimodziyo, mitengo yonse yamʼnkhalango ifuule mosangalala+