Salimo 97:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Sangalalani chifukwa cha Yehova, olungama inu,Ndipo yamikirani dzina lake loyera.*