Salimo 98:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye wakumbukira chikondi chake chokhulupirika komanso kukhulupirika kumene analonjeza nyumba ya Isiraeli.+ Anthu onse padziko lapansi aona mmene Mulungu wathu wapulumutsira anthu ake.*+
3 Iye wakumbukira chikondi chake chokhulupirika komanso kukhulupirika kumene analonjeza nyumba ya Isiraeli.+ Anthu onse padziko lapansi aona mmene Mulungu wathu wapulumutsira anthu ake.*+