Salimo 99:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iwo atamande dzina lanu lalikulu,+Chifukwa ndi lochititsa mantha komanso loyera.