Salimo 99:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu Yehova Mulungu wathu munawayankha.+ Inu ndi Mulungu amene munawakhululukira,+Koma munawalanga chifukwa cha machimo awo.+
8 Inu Yehova Mulungu wathu munawayankha.+ Inu ndi Mulungu amene munawakhululukira,+Koma munawalanga chifukwa cha machimo awo.+