-
Salimo 101:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
101 Ndidzaimba za chikondi chokhulupirika komanso chilungamo chanu.
Inu Yehova, ndidzakuimbirani nyimbo zokutamandani.
-