Salimo 101:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Sindidzayangʼana chinthu chilichonse choipa.* Ndimadana ndi zochita za anthu amene asiya kuchita zinthu zabwino.+Sindidzalola kuti zochita zawozo zindikhudze. Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 101:3 Nsanja ya Olonda,7/15/2011, tsa. 13
3 Sindidzayangʼana chinthu chilichonse choipa.* Ndimadana ndi zochita za anthu amene asiya kuchita zinthu zabwino.+Sindidzalola kuti zochita zawozo zindikhudze.