Salimo 102:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mtima wanga wakhala ngati udzu umene wawauka nʼkuuma,+Chifukwa sindikulakalaka kudya chakudya.