Salimo 102:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndikudya phulusa ngati chakudya,+Ndipo zakumwa zanga ndi zosakanikirana ndi misozi.+