Salimo 102:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndithudi inu mudzanyamuka nʼkusonyeza Ziyoni chifundo,+Chifukwa imeneyi ndi nthawi yoti mumusonyeze kukoma mtima kwanu.+Nthawi yoikidwiratu yakwana.+
13 Ndithudi inu mudzanyamuka nʼkusonyeza Ziyoni chifundo,+Chifukwa imeneyi ndi nthawi yoti mumusonyeze kukoma mtima kwanu.+Nthawi yoikidwiratu yakwana.+