Salimo 102:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mitundu ya anthu idzaopa dzina lanu, inu Yehova,Ndipo mafumu onse apadziko lapansi adzaopa ulemerero wanu.+
15 Mitundu ya anthu idzaopa dzina lanu, inu Yehova,Ndipo mafumu onse apadziko lapansi adzaopa ulemerero wanu.+