Salimo 102:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Adzamvetsera pemphero la anthu osauka.+Iye sadzapeputsa pemphero lawo.+