Salimo 102:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ine ndinati: “Inu Mulungu wanga,Musachotse moyo wanga ndisanakalambe,Inu amene mudzakhalapo ku mibadwo yonse.+
24 Ine ndinati: “Inu Mulungu wanga,Musachotse moyo wanga ndisanakalambe,Inu amene mudzakhalapo ku mibadwo yonse.+