Salimo 104:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Amatulutsa madzi mu akasupe kuti apite mʼzigwa*Ndipo madziwo amadutsa pakati pa mapiri.