Salimo 104:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mitengo ya Yehova imalandira madzi okwanira,Mikungudza ya ku Lebanoni imene iye anadzala,