Salimo 104:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mbalame zimamanga zisa zawo mmenemo. Nyumba ya dokowe+ imakhala mʼmitengo ya junipa.*