Salimo 104:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mumabweretsa mdima ndipo usiku umayamba,+Nthawi imene nyama zonse zakutchire zimayendayenda.