Salimo 105:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Wakumbukira pangano limene anapangana ndi Abulahamu,+Komanso lumbiro limene analumbira kwa Isaki,+