Salimo 106:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Makolo athu ku Iguputo, sanayamikire* ntchito zanu zodabwitsa. Sanakumbukire chikondi chanu chokhulupirika chomwe ndi chochuluka,Koma anapanduka panyanja, pafupi ndi Nyanja Yofiira.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 106:7 Nsanja ya Olonda,9/1/1995, ptsa. 19-203/15/1989, tsa. 17
7 Makolo athu ku Iguputo, sanayamikire* ntchito zanu zodabwitsa. Sanakumbukire chikondi chanu chokhulupirika chomwe ndi chochuluka,Koma anapanduka panyanja, pafupi ndi Nyanja Yofiira.+