Salimo 106:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma Mulungu anawapulumutsa kuti dzina lake lilemekezedwe,+Kuti mphamvu zake zidziwike.+