Salimo 106:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mulungu anawapatsa zimene anapempha,Koma anawagwetsera matenda amene anawachititsa kuti awonde kwambiri.+
15 Mulungu anawapatsa zimene anapempha,Koma anawagwetsera matenda amene anawachititsa kuti awonde kwambiri.+