Salimo 106:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Iwo anamukwiyitsa chifukwa cha zochita zawo,+Ndipo pakati pawo panagwa mliri.+