Salimo 106:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Pofuna kuwathandiza iye ankakumbukira pangano lake,Ndipo ankawamvera chisoni* chifukwa cha chikondi chake chokhulupirika chomwe ndi chachikulu.*+
45 Pofuna kuwathandiza iye ankakumbukira pangano lake,Ndipo ankawamvera chisoni* chifukwa cha chikondi chake chokhulupirika chomwe ndi chachikulu.*+