Salimo 107:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Anthuwo amafesa mbewu nʼkulima minda ya mpesa,+Kuti akhale ndi zokolola.+