Salimo 107:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Mulungu amawadalitsa ndipo amachuluka kwambiri.Iye salola kuti ngʼombe zawo zichepe.+