Salimo 108:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Dzuka, iwe choimbira cha zingwe, ndi iwenso zeze.+ Ine ndidzadzuka mʼbandakucha.