Salimo 109:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Akamaweruzidwa apezeke kuti ndi wolakwa.*Ndipo ngakhale pemphero lake lizionedwa ngati tchimo.+