-
Salimo 109:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Alekeni anditemberere, koma inu mundipatse madalitso.
Iwo akaimirira kuti andiukire, inu muwachititse manyazi,
Koma lolani ine mtumiki wanu kuti ndisangalale.
-