Salimo 111:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chiyambi cha nzeru ndi kuopa Yehova.+ ש [Sin] Onse otsatira malamulo ake amasonyeza kuti ndi ozindikira.+ ת [Taw] Iye ayenera kutamandidwa mpaka kalekale. Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 111:10 Nsanja ya Olonda,3/15/2009, tsa. 243/15/1995, tsa. 16 Kukambitsirana, tsa. 136
10 Chiyambi cha nzeru ndi kuopa Yehova.+ ש [Sin] Onse otsatira malamulo ake amasonyeza kuti ndi ozindikira.+ ת [Taw] Iye ayenera kutamandidwa mpaka kalekale.