Salimo 112:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kwa anthu owongoka mtima iye amawala ngati kuwala kumene kumaunika mumdima.+ ח [Heth] Iye ndi wokoma mtima,* wachifundo+ komanso wolungama. Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 112:4 Nsanja ya Olonda,3/15/2009, ptsa. 26-27
4 Kwa anthu owongoka mtima iye amawala ngati kuwala kumene kumaunika mumdima.+ ח [Heth] Iye ndi wokoma mtima,* wachifundo+ komanso wolungama.