Salimo 112:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Woipa adzaona zimenezi ndipo adzakhumudwa. ש [Shin] Adzakukuta mano ndi kusungunuka. ת [Taw] Zimene anthu oipa amalakalaka sizidzachitika.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 112:10 Nsanja ya Olonda,3/15/2009, tsa. 28
10 Woipa adzaona zimenezi ndipo adzakhumudwa. ש [Shin] Adzakukuta mano ndi kusungunuka. ת [Taw] Zimene anthu oipa amalakalaka sizidzachitika.+