Salimo 113:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndi ndani angafanane ndi Yehova Mulungu wathu,+Amene amakhala* pamwamba?