Salimo 115:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Inu nyumba ya Aroni,+ khulupirirani Yehova,Iye ndi amene amakuthandizani komanso ndi chishango chanu.
10 Inu nyumba ya Aroni,+ khulupirirani Yehova,Iye ndi amene amakuthandizani komanso ndi chishango chanu.