Salimo 116:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu mwandipulumutsa ku imfa,Mwapukuta misozi yanga ndipo mwateteza phazi langa kuti lisapunthwe.+