Salimo 116:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndidzamwa zamʼkapu yachipulumutso,*Ndipo ndidzaitana pa dzina la Yehova.