Salimo 116:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndikukupemphani, inu Yehova,Chifukwa ine ndi mtumiki wanu. Ndine mtumiki wanu, mwana wa kapolo wanu wamkazi. Mwamasula zingwe zimene anandimanga nazo.+
16 Ndikukupemphani, inu Yehova,Chifukwa ine ndi mtumiki wanu. Ndine mtumiki wanu, mwana wa kapolo wanu wamkazi. Mwamasula zingwe zimene anandimanga nazo.+