Salimo 118:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Inandizungulira ngati njuchi,Koma inathimitsidwa mwamsanga ngati moto umene uli pakati pa minga. Mʼdzina la Yehova,Ndinaithamangitsira kutali.+
12 Inandizungulira ngati njuchi,Koma inathimitsidwa mwamsanga ngati moto umene uli pakati pa minga. Mʼdzina la Yehova,Ndinaithamangitsira kutali.+