Salimo 118:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Yehova ndi Mulungu.Iye amatipatsa kuwala.+ Tiyeni tikhale limodzi ndi gulu la anthu amene akupita kuchikondwerero atanyamula nthambi mʼmanja mwawo,+Mpaka kukafika panyanga za guwa lansembe.+
27 Yehova ndi Mulungu.Iye amatipatsa kuwala.+ Tiyeni tikhale limodzi ndi gulu la anthu amene akupita kuchikondwerero atanyamula nthambi mʼmanja mwawo,+Mpaka kukafika panyanga za guwa lansembe.+