Salimo 118:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Inu ndinu Mulungu wanga ndipo ndidzakutamandani.Ndinu Mulungu wanga ndipo ndidzakukwezani.+