Salimo 119:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 119 Osangalala ndi anthu amene salakwitsa kanthu* mʼnjira zawo,Amene amatsatira chilamulo cha Yehova.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 119:1 Nsanja ya Olonda,4/15/2005, tsa. 10
119 Osangalala ndi anthu amene salakwitsa kanthu* mʼnjira zawo,Amene amatsatira chilamulo cha Yehova.+