Salimo 119:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mumadzudzula anthu odzikuza,Otembereredwa amene akusochera nʼkusiya kutsatira malamulo anu.+