Salimo 119:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndagona pafumbi.+ Ndithandizeni kuti ndikhalebe ndi moyo mogwirizana ndi mawu anu.+