Salimo 119:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ine ndasankha kuti ndizichita zinthu mokhulupirika.+ Ndimadziwa kuti zigamulo zanu ndi zolungama.