Salimo 119:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ndidzatsatira* malamulo anu ndi mtima wonse,Chifukwa mwandithandiza kuti ndiwamvetse bwino.