Salimo 119:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Ndithandizeni kuti ndipitirize kunena mawu a choonadi,Chifukwa ndikuyembekezera* chigamulo chanu.