Salimo 119:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Kumbukirani mawu amene* munandiuza ine mtumiki wanu,Mawu amene mumandipatsa nawo chiyembekezo.*